Genesis 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mulungu anakhalabe ndi Isimaeli.+ Mnyamata ameneyu anali kukhala m’chipululu, ndipo anakula n’kukhala katswiri woponya muvi ndi uta.+
20 Mulungu anakhalabe ndi Isimaeli.+ Mnyamata ameneyu anali kukhala m’chipululu, ndipo anakula n’kukhala katswiri woponya muvi ndi uta.+