Ekisodo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Koma iwe patula Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake pakati pa ana a Isiraeli, ndipo Aroniyo+ atumikire monga wansembe wanga pamodzi ndi ana akewo,+ Nadabu, Abihu,+ Eleazara ndi Itamara.+ 2 Mbiri 35:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho iye anaika ansembe pa ntchito zawo+ ndipo anawalimbikitsa+ pa utumiki wawo wa panyumba ya Yehova.+
28 “Koma iwe patula Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake pakati pa ana a Isiraeli, ndipo Aroniyo+ atumikire monga wansembe wanga pamodzi ndi ana akewo,+ Nadabu, Abihu,+ Eleazara ndi Itamara.+
2 Choncho iye anaika ansembe pa ntchito zawo+ ndipo anawalimbikitsa+ pa utumiki wawo wa panyumba ya Yehova.+