Levitiko 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu akapanga lonjezo lapadera+ lopereka munthu mnzake kwa Yehova pa mtengo woikidwiratu, Levitiko 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo wansembe azinena mtengo wake. Mtengowo uzidalira mmene nyamayo ilili, kaya ndi yabwino kapena yoipa. Mtengo wa nyamayo+ umene wansembe wanena uzikhala womwewo.
2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu akapanga lonjezo lapadera+ lopereka munthu mnzake kwa Yehova pa mtengo woikidwiratu,
12 Ndipo wansembe azinena mtengo wake. Mtengowo uzidalira mmene nyamayo ilili, kaya ndi yabwino kapena yoipa. Mtengo wa nyamayo+ umene wansembe wanena uzikhala womwewo.