Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘Munthu aliyense, mwamuna kapena mkazi, akachita lonjezo lapadera lokhala Mnaziri+ kwa Yehova,

  • Deuteronomo 23:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Ukapereka lonjezo kwa Yehova+ Mulungu wako usachedwe kulikwaniritsa kuopera kuti ungachimwe,+ chifukwa Yehova Mulungu wako adzafuna ndithu kuti ukwaniritse chimene walonjezacho.+

  • Oweruza 11:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndiyeno Yefita analonjeza+ Yehova kuti: “Ngati mudzaperekadi ana a Amoni m’manja mwanga,

  • 1 Samueli 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iye anayamba kulonjeza+ kuti: “Inu Yehova wa makamu, mukaona nsautso yanga, ine kapolo wanu wamkazi,+ ndi kundikumbukira,+ ndiponso ngati simudzaiwala kapolo wanu wamkazi ndi kum’patsa mwana wamwamuna, ndidzam’pereka kwa Yehova masiku onse a moyo wake, ndipo lezala silidzadutsa m’mutu mwake.”+

  • Mlaliki 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa palibe amene amasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena