Numeri 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+ Salimo 66:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzalowa m’nyumba yanu ndi nsembe zopsereza zathunthu.+Ine ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa inu+ Salimo 116:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa Yehova,+Ndidzawakwaniritsa pamaso pa anthu ake onse,+ Yona 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ine, ndidzakutamandani ndi kupereka nsembe kwa inu.+Zimene ndalonjeza ndidzazikwaniritsa.+ Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.”+ Mabuku a Chichewa (1974-2025) Tulukani Lowani Chichewa Tumizirani Ena Zimene Mumakonda Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania Zoyenera Kutsatira Nkhani Yosunga Chinsinsi Privacy Settings JW.ORG Lowani Tumizirani Ena Tumizirani Wina pa Imelo
2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+
13 Ndidzalowa m’nyumba yanu ndi nsembe zopsereza zathunthu.+Ine ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa inu+ Salimo 116:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa Yehova,+Ndidzawakwaniritsa pamaso pa anthu ake onse,+ Yona 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ine, ndidzakutamandani ndi kupereka nsembe kwa inu.+Zimene ndalonjeza ndidzazikwaniritsa.+ Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.”+
18 Ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa Yehova,+Ndidzawakwaniritsa pamaso pa anthu ake onse,+ Yona 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ine, ndidzakutamandani ndi kupereka nsembe kwa inu.+Zimene ndalonjeza ndidzazikwaniritsa.+ Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.”+
9 Koma ine, ndidzakutamandani ndi kupereka nsembe kwa inu.+Zimene ndalonjeza ndidzazikwaniritsa.+ Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.”+