Genesis 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yakobo analonjeza+ kuti: “Ndithu ngati Mulungu adzakhalabe nane n’kundisungabe pa ulendo wangawu, ndiponso ngati adzandipatsadi chakudya ndi zovala,+ Levitiko 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu akapanga lonjezo lapadera+ lopereka munthu mnzake kwa Yehova pa mtengo woikidwiratu, Oweruza 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Yefita analonjeza+ Yehova kuti: “Ngati mudzaperekadi ana a Amoni m’manja mwanga,
20 Yakobo analonjeza+ kuti: “Ndithu ngati Mulungu adzakhalabe nane n’kundisungabe pa ulendo wangawu, ndiponso ngati adzandipatsadi chakudya ndi zovala,+
2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu akapanga lonjezo lapadera+ lopereka munthu mnzake kwa Yehova pa mtengo woikidwiratu,