Salimo 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chifukwa cha zimene mwachita ndidzakutamandani mumpingo waukulu.+Ndidzakwaniritsa malonjezo anga pamaso pa anthu oopa iye.+ Salimo 56:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Mulungu, ine ndikuyenera kukwaniritsa malonjezo anga kwa inu.+Ndidzapereka kwa inu nsembe zoyamikira.+ Salimo 116:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa Yehova,+Pamaso pa anthu ake onse. Mlaliki 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa palibe amene amasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+
25 Chifukwa cha zimene mwachita ndidzakutamandani mumpingo waukulu.+Ndidzakwaniritsa malonjezo anga pamaso pa anthu oopa iye.+
12 Inu Mulungu, ine ndikuyenera kukwaniritsa malonjezo anga kwa inu.+Ndidzapereka kwa inu nsembe zoyamikira.+
4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa palibe amene amasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+