3 popereka nsembe yotentha ndi moto kwa Yehova,+ kuti ikhale nsembe yopsereza,+ kapena nsembe yochitira lonjezo lapadera, kapena nsembe yongopereka mwaufulu,+ kapena yopereka pa nthawi ya zikondwerero zanu,+ kuti mufukize fungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova+ la nyama ya ng’ombe kapena ya nkhosa,