Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 23:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “‘Zikondwerero+ za Yehova, kapena kuti misonkhano yopatulika+ imene muyenera kulengeza pa nthawi yake yoikidwiratu+ ndi iyi:

  • Numeri 28:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “‘M’mwezi woyamba, pa tsiku la 14, pazikhala pasika wa Yehova.+

  • Numeri 29:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “‘Pa tsiku loyamba la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse.+ Lizikhala tsiku lanu loliza lipenga.+

  • Deuteronomo 16:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Uzichita chikondwerero cha misasa+ masiku 7, potuta zokolola kuchokera pamalo opunthira mbewu, pamalo oyengera mafuta ndi pamalo opondera mphesa.

  • Deuteronomo 16:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Mwamuna aliyense pakati panu azikaonekera katatu pa chaka pamaso pa Yehova Mulungu wanu, pamalo amene Mulungu adzasankhe.+ Azikaonekera pa chikondwerero cha mkate wopanda chofufumitsa,+ chikondwerero cha masabata+ ndi pa chikondwerero cha misasa.+ Palibe amene ayenera kuonekera kwa Yehova chimanjamanja.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena