Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 30:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Komabe, ngati mkazi walonjeza ali m’nyumba ya mwamuna wake, kapena ngati wachita lonjezo lodzimana+ mwa kulumbirira moyo wake,

  • Salimo 132:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Kumbukirani kuti analumbira kwa inu Yehova,+

      Analonjeza kwa Wamphamvu+ wa Yakobo kuti:+

  • Numeri 30:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 mwamuna wake n’kumva koma osanenapo kanthu, osam’kaniza, malonjezo ake onse akhale momwemo, ndipo lonjezo lililonse lodzimana limene walumbirira moyo wake likhale momwemo.

  • Machitidwe 23:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chotero anapita kwa ansembe aakulu+ ndi kwa akulu kukanena kuti: “Ife tachita lumbiro ndi kudzitemberera kuti sitilawa chakudya kufikira titapha Paulo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena