Salimo 56:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Mulungu, ine ndikuyenera kukwaniritsa malonjezo anga kwa inu.+Ndidzapereka kwa inu nsembe zoyamikira.+ Salimo 65:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Inu Mulungu, anthu akukutamandani mu Ziyoni+ ndipo akhala chete pamaso panu,Iwo adzakwaniritsa malonjezo awo kwa inu.+
12 Inu Mulungu, ine ndikuyenera kukwaniritsa malonjezo anga kwa inu.+Ndidzapereka kwa inu nsembe zoyamikira.+
65 Inu Mulungu, anthu akukutamandani mu Ziyoni+ ndipo akhala chete pamaso panu,Iwo adzakwaniritsa malonjezo awo kwa inu.+