2 Samueli 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Natani anauza mfumu kuti: “Chitani chilichonse chimene chili mumtima mwanu,+ chifukwa Yehova ali nanu.” Salimo 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chifukwa cha zimene mwachita ndidzakutamandani mumpingo waukulu.+Ndidzakwaniritsa malonjezo anga pamaso pa anthu oopa iye.+ Salimo 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.] Salimo 61:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu mpaka muyaya,+Kuti ndikwaniritse malonjezo anga tsiku ndi tsiku.+ Salimo 146:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wodala ndi munthu amene thandizo lake limachokera kwa Mulungu wa Yakobo,+Amene chiyembekezo chake chili mwa Yehova Mulungu wake,+
3 Pamenepo Natani anauza mfumu kuti: “Chitani chilichonse chimene chili mumtima mwanu,+ chifukwa Yehova ali nanu.”
25 Chifukwa cha zimene mwachita ndidzakutamandani mumpingo waukulu.+Ndidzakwaniritsa malonjezo anga pamaso pa anthu oopa iye.+
11 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.]
8 Choncho ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu mpaka muyaya,+Kuti ndikwaniritse malonjezo anga tsiku ndi tsiku.+
5 Wodala ndi munthu amene thandizo lake limachokera kwa Mulungu wa Yakobo,+Amene chiyembekezo chake chili mwa Yehova Mulungu wake,+