1 Mafumu 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo bambo anga Davide, anafuna mumtima mwawo kumanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+ 1 Mbiri 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Natani anauza Davide kuti: “Chitani chilichonse chimene chili mumtima mwanu,+ chifukwa Mulungu woona ali nanu.”+ 1 Mbiri 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo Davide anauza mwana wake Solomo kuti: “Ineyo, ndinafunitsitsa ndi mtima wanga wonse+ kumanga nyumba ya dzina+ la Yehova Mulungu wanga.
17 Ndipo bambo anga Davide, anafuna mumtima mwawo kumanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+
2 Pamenepo Natani anauza Davide kuti: “Chitani chilichonse chimene chili mumtima mwanu,+ chifukwa Mulungu woona ali nanu.”+
7 Ndipo Davide anauza mwana wake Solomo kuti: “Ineyo, ndinafunitsitsa ndi mtima wanga wonse+ kumanga nyumba ya dzina+ la Yehova Mulungu wanga.