2 Samueli 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Natani anauza mfumu kuti: “Chitani chilichonse chimene chili mumtima mwanu,+ chifukwa Yehova ali nanu.”
3 Pamenepo Natani anauza mfumu kuti: “Chitani chilichonse chimene chili mumtima mwanu,+ chifukwa Yehova ali nanu.”