1 Mafumu 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo bambo anga Davide ankafunitsitsa kumanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+