2 Samueli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 inauza Natani+ mneneri kuti: “Tsopano taona, ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la Mulungu woona likukhala m’chihema chansalu.”+ 1 Mbiri 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Natani anauza Davide kuti: “Chitani chilichonse chimene chili mumtima mwanu,+ chifukwa Mulungu woona ali nanu.”+
2 inauza Natani+ mneneri kuti: “Tsopano taona, ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la Mulungu woona likukhala m’chihema chansalu.”+
2 Pamenepo Natani anauza Davide kuti: “Chitani chilichonse chimene chili mumtima mwanu,+ chifukwa Mulungu woona ali nanu.”+