2 Samueli 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno analowetsa likasa la Yehova muhema limene Davide anamanga n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako Davide anapereka kwa Yehova nsembe zopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano.+ 1 Mbiri 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide anapitiriza kumanga nyumba+ zake mu Mzinda wa Davide, ndipo anakonza malo+ oikapo likasa la Mulungu woona, n’kulimangira hema. 1 Mbiri 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Motero analowetsa+ likasa la Mulungu woona muhema limene Davide anamanga, n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano kwa Mulungu woona.+
17 Ndiyeno analowetsa likasa la Yehova muhema limene Davide anamanga n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako Davide anapereka kwa Yehova nsembe zopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano.+
15 Davide anapitiriza kumanga nyumba+ zake mu Mzinda wa Davide, ndipo anakonza malo+ oikapo likasa la Mulungu woona, n’kulimangira hema.
16 Motero analowetsa+ likasa la Mulungu woona muhema limene Davide anamanga, n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano kwa Mulungu woona.+