1 Mbiri 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Motero analowetsa+ likasa la Mulungu woona muhema limene Davide anamanga, n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano kwa Mulungu woona.+ Salimo 132:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kufikira Yehova nditamupezera nyumba,+Kufikira nditapeza chihema chachikulu cha Wamphamvu wa Yakobo.”+ Machitidwe 7:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu anakomera mtima+ Davide ndipo iye anapempha mwayi wakuti amange nyumba yokhalamo+ Mulungu wa Yakobo.
16 Motero analowetsa+ likasa la Mulungu woona muhema limene Davide anamanga, n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano kwa Mulungu woona.+
5 Kufikira Yehova nditamupezera nyumba,+Kufikira nditapeza chihema chachikulu cha Wamphamvu wa Yakobo.”+
46 Mulungu anakomera mtima+ Davide ndipo iye anapempha mwayi wakuti amange nyumba yokhalamo+ Mulungu wa Yakobo.