Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 inauza Natani+ mneneri kuti: “Tsopano taona, ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la Mulungu woona likukhala m’chihema chansalu.”+

  • 1 Mbiri 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Davide anasonkhanitsa Aisiraeli onse ku Yerusalemu+ kuti akanyamule likasa+ la Yehova, kupita nalo kumalo amene iye anakonza kuti akaliike.

  • 1 Mbiri 15:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano Davide anawauza kuti: “Inuyo ndinu atsogoleri+ a nyumba ya makolo a Alevi. Choncho inu ndi abale anu mudziyeretse,+ ndipo mukatenge likasa la Yehova Mulungu wa Isiraeli n’kukaliika kumalo amene ine ndakonza kuti likakhaleko.

  • Machitidwe 7:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Mulungu anakomera mtima+ Davide ndipo iye anapempha mwayi wakuti amange nyumba yokhalamo+ Mulungu wa Yakobo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena