2 Samueli 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Yehova anatuma Natani+ kwa Davide. Natani atafika kwa Davide+ anamuuza kuti: “Panali amuna awiri amene anali kukhala mumzinda umodzi. Wina anali wolemera ndipo wina anali wosauka. 1 Mbiri 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zokhudza Davide mfumu, zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa pakati pa mawu a Samueli wamasomphenya,*+ Natani+ mneneri, ndiponso pakati pa mawu a Gadi+ wamasomphenya.
12 Tsopano Yehova anatuma Natani+ kwa Davide. Natani atafika kwa Davide+ anamuuza kuti: “Panali amuna awiri amene anali kukhala mumzinda umodzi. Wina anali wolemera ndipo wina anali wosauka.
29 Nkhani zokhudza Davide mfumu, zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa pakati pa mawu a Samueli wamasomphenya,*+ Natani+ mneneri, ndiponso pakati pa mawu a Gadi+ wamasomphenya.