1 Mbiri 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zokhudza Mfumu Davide, kuyambira pachiyambi mpaka kumapeto, zikupezeka mʼzinthu zimene analemba Samueli wamasomphenya,* mneneri Natani+ ndiponso Gadi+ wamasomphenya. 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:29 Nsanja ya Olonda,3/15/2009, tsa. 32
29 Nkhani zokhudza Mfumu Davide, kuyambira pachiyambi mpaka kumapeto, zikupezeka mʼzinthu zimene analemba Samueli wamasomphenya,* mneneri Natani+ ndiponso Gadi+ wamasomphenya.