1 Mbiri 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero, Davide anasonkhanitsa+ Aisiraeli onse kuchokera kumtsinje wa Iguputo+ mpaka kukafika polowera ku Hamati,+ kuti akatenge likasa+ la Mulungu woona ku Kiriyati-yearimu.+
5 Chotero, Davide anasonkhanitsa+ Aisiraeli onse kuchokera kumtsinje wa Iguputo+ mpaka kukafika polowera ku Hamati,+ kuti akatenge likasa+ la Mulungu woona ku Kiriyati-yearimu.+