Numeri 34:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuchokera kuphiri la Hora, mukalembe malirewo akafike ku Hamati,+ mpaka ku Zedadi.+ Zekariya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mawu amenewa akuweruzanso Hamati+ amene anachita naye malire. Komanso akuweruza Turo+ ndi Sidoni+ chifukwa ali ndi nzeru zambiri.+
2 Mawu amenewa akuweruzanso Hamati+ amene anachita naye malire. Komanso akuweruza Turo+ ndi Sidoni+ chifukwa ali ndi nzeru zambiri.+