Yeremiya 49:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uthenga wokhudza Damasiko+ ndi wonena kuti: “Hamati+ ndi Aripadi+ achita manyazi chifukwa chakuti amva uthenga woipa. Iwo apasuka+ ndipo nyanja yawinduka, moti singathe kukhala bata.+ Amosi 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yehova, Mulungu wa makamu wanena kuti, ‘Inu a m’nyumba ya Isiraeli, ine ndikukudzutsirani mtundu wa anthu+ umene udzakuponderezani kuyambira kumalire ndi Hamati+ mpaka kuchigwa cha Araba.’”
23 Uthenga wokhudza Damasiko+ ndi wonena kuti: “Hamati+ ndi Aripadi+ achita manyazi chifukwa chakuti amva uthenga woipa. Iwo apasuka+ ndipo nyanja yawinduka, moti singathe kukhala bata.+
14 Tsopano Yehova, Mulungu wa makamu wanena kuti, ‘Inu a m’nyumba ya Isiraeli, ine ndikukudzutsirani mtundu wa anthu+ umene udzakuponderezani kuyambira kumalire ndi Hamati+ mpaka kuchigwa cha Araba.’”