Numeri 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho amunawo anapita kukazonda dzikolo, kuyambira kuchipululu cha Zini+ mpaka ku Rehobu,+ kufupi ndi Hamati.+ 2 Mafumu 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako mfumu ya Asuri inatenga anthu kuchokera ku Babulo,+ Kuta, Ava,+ Hamati,+ ndi Sefaravaimu+ n’kuwakhazika m’mizinda ya Samariya,+ m’malo mwa ana a Isiraeli. Anthuwo anatenga Samariya n’kumakhala m’mizinda yake. Yesaya 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi Kalino+ sali ngati Karikemisi?+ Kodi Hamati+ sali ngati Aripadi?+ Kodi Samariya+ sali ngati Damasiko?+ Zekariya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mawu amenewa akuweruzanso Hamati+ amene anachita naye malire. Komanso akuweruza Turo+ ndi Sidoni+ chifukwa ali ndi nzeru zambiri.+
21 Choncho amunawo anapita kukazonda dzikolo, kuyambira kuchipululu cha Zini+ mpaka ku Rehobu,+ kufupi ndi Hamati.+
24 Kenako mfumu ya Asuri inatenga anthu kuchokera ku Babulo,+ Kuta, Ava,+ Hamati,+ ndi Sefaravaimu+ n’kuwakhazika m’mizinda ya Samariya,+ m’malo mwa ana a Isiraeli. Anthuwo anatenga Samariya n’kumakhala m’mizinda yake.
9 Kodi Kalino+ sali ngati Karikemisi?+ Kodi Hamati+ sali ngati Aripadi?+ Kodi Samariya+ sali ngati Damasiko?+
2 Mawu amenewa akuweruzanso Hamati+ amene anachita naye malire. Komanso akuweruza Turo+ ndi Sidoni+ chifukwa ali ndi nzeru zambiri.+