Amosi 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pitani mukaone ku Kaline ndipo kuchokera kumeneko mukapite ku Hamati+ kumene kuli anthu ambiri, kenako mukapite ku Gati+ wa Afilisiti. Kodi mizinda imeneyi imaposa maufumu anu awiriwa?* Kapena kodi malo awo ndi aakulu kuposa malo anu?+
2 Pitani mukaone ku Kaline ndipo kuchokera kumeneko mukapite ku Hamati+ kumene kuli anthu ambiri, kenako mukapite ku Gati+ wa Afilisiti. Kodi mizinda imeneyi imaposa maufumu anu awiriwa?* Kapena kodi malo awo ndi aakulu kuposa malo anu?+