Yesaya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi iliyonse imene dzanja langa lafikira maufumu olambira milungu yopanda phindu, omwe zifaniziro zawo zogoba n’zambiri kuposa zimene zili ku Yerusalemu ndi ku Samariya,+ Nahumu 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi iwe uli pabwino kuposa No-amoni+ amene anali pafupi ndi ngalande zochokera mumtsinje wa Nailo?+ Iye anali wozunguliridwa ndi madzi. Chuma chake chinali kuchokera m’nyanja, ndipo nyanjayo ndiyo inali khoma lake.
10 Nthawi iliyonse imene dzanja langa lafikira maufumu olambira milungu yopanda phindu, omwe zifaniziro zawo zogoba n’zambiri kuposa zimene zili ku Yerusalemu ndi ku Samariya,+
8 Kodi iwe uli pabwino kuposa No-amoni+ amene anali pafupi ndi ngalande zochokera mumtsinje wa Nailo?+ Iye anali wozunguliridwa ndi madzi. Chuma chake chinali kuchokera m’nyanja, ndipo nyanjayo ndiyo inali khoma lake.