Yesaya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzanja langa lagwira maufumu olambira milungu yopanda phindu,Amene zifaniziro zawo zogoba zinali zambiri kuposa za ku Yerusalemu ndi ku Samariya.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:10 Yesaya 1, ptsa. 146-147
10 Dzanja langa lagwira maufumu olambira milungu yopanda phindu,Amene zifaniziro zawo zogoba zinali zambiri kuposa za ku Yerusalemu ndi ku Samariya.+