Yesaya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi iliyonse imene dzanja langa lafikira maufumu olambira milungu yopanda phindu, omwe zifaniziro zawo zogoba n’zambiri kuposa zimene zili ku Yerusalemu ndi ku Samariya,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:10 Yesaya 1, ptsa. 146-147
10 Nthawi iliyonse imene dzanja langa lafikira maufumu olambira milungu yopanda phindu, omwe zifaniziro zawo zogoba n’zambiri kuposa zimene zili ku Yerusalemu ndi ku Samariya,+