Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 18:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Kodi milungu ya Hamati+ ndi Aripadi+ ili kuti? Ili kuti milungu ya Sefaravaimu,+ Hena,+ ndi Iva?+ Kodi yalanditsa Samariya m’manja mwanga?+

  • 2 Mafumu 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Atentha milungu yawo pamoto, chifukwa sinali milungu,+ koma ntchito ya manja a anthu,+ mitengo ndi miyala, n’chifukwa chake anaiwononga.

  • 2 Mbiri 32:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Anapitiriza kulankhula monyoza+ Mulungu wa Yerusalemu+ mofanana ndi mmene ankanyozera milungu ya mitundu ya anthu a padziko lapansi, yopangidwa ndi manja a anthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena