Salimo 76:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malo ake opumulirako ali ku Salemu,+Malo ake okhalamo ali ku Ziyoni.+ Salimo 132:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wasankha Ziyoni,+Ndipo amafunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye amati:+