Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Kumeneko mudzatumikira milungu+ yopangidwa ndi manja a anthu, milungu ya mtengo ndi mwala,+ imene siingaone, kumva, kudya kapena kununkhiza.+

  • 2 Mafumu 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Atentha milungu yawo pamoto, chifukwa sinali milungu,+ koma ntchito ya manja a anthu,+ mitengo ndi miyala, n’chifukwa chake anaiwononga.

  • Salimo 135:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mafano a anthu a mitundu ina ndi opangidwa ndi siliva ndi golide,+

      Ntchito ya manja a munthu wochokera kufumbi.+

  • Yesaya 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo. Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga.+

  • Hoseya 8:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Zimenezi zachokera ku Isiraeli.+ Mmisiri ndiye anapanga fano la mwana wa ng’ombe la ku Samariya.+ Fanolo si Mulungu woona, chifukwa lidzangokhala ngati nkhuni zowazawaza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena