Ezekieli 28:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana ku Sidoni+ ndipo ulosere zoipa zimene zidzamuchitikire.