Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 23:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Chita manyazi iwe Sidoni,+ ndiponso iwe malo achitetezo a m’mbali mwa nyanja, chifukwa nyanja yanena kuti: “Sindinamvepo zowawa za pobereka, ndipo sindinaberekepo. Sindinalerepo anyamata kapena anamwali.”+

  • Yeremiya 25:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 mafumu onse a Turo,+ mafumu onse a Sidoni+ ndi mafumu a pachilumba cha m’nyanja.

  • Ezekieli 32:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 “‘Kumeneko n’kumene kuli nduna zonse za kumpoto. Kulinso Asidoni+ onse amene anatsikira kumanda ali amanyazi. Anatsikira kumeneko limodzi ndi ophedwa, ngakhale kuti anali ochititsa mantha chifukwa cha mphamvu zawo. Adzagona m’manda limodzi ndi ophedwa ndi lupanga ali osadulidwa. Iwo adzachita manyazi pamodzi ndi otsikira kudzenje.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena