-
Ezekieli 32:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 “‘Kumeneko n’kumene kuli nduna zonse za kumpoto. Kulinso Asidoni+ onse amene anatsikira kumanda ali amanyazi. Anatsikira kumeneko limodzi ndi ophedwa, ngakhale kuti anali ochititsa mantha chifukwa cha mphamvu zawo. Adzagona m’manda limodzi ndi ophedwa ndi lupanga ali osadulidwa. Iwo adzachita manyazi pamodzi ndi otsikira kudzenje.+
-