Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 14:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Fuula chipata iwe! Lira mokweza mzinda iwe! Nonsenu mudzataya mtima, inu anthu okhala m’Filisitiya! Pakuti utsi ukubwera kuchokera kumpoto, ndipo palibe msilikali amene akutsalira pa magulu ake ankhondo.”+

  • Yeremiya 25:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 khamu lonse la anthu a mitundu yosiyanasiyana, mafumu onse a dziko la Uzi,+ mafumu onse a dziko la Afilisiti,+ Asikeloni,+ Gaza,+ Ekironi+ ndi otsala onse a ku Asidodi,+

  • Amosi 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndidzapha anthu a ku Asidodi+ pamodzi ndi wogwira ndodo yachifumu wa ku Asikeloni.+ Ndidzalanga+ Ekironi+ ndipo ndidzafafaniza otsala mwa Afilisiti,”+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’

  • Zefaniya 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Tsoka kwa anthu okhala m’chigawo cha m’mphepete mwa nyanja, mtundu wa Akereti.+ Yehova wakudzudzulani anthu inu. Iwe Kanani, dziko la Afilisiti, nawenso ndidzakuwononga, kotero kuti m’dziko lako simudzatsala munthu aliyense.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena