Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mesa+ mfumu ya Mowabu anali woweta nkhosa. Ankapereka kwa mfumu ya Isiraeli ana a nkhosa 100,000, ndi nkhosa zamphongo zosameta ubweya zokwana 100,000 monga msonkho.

  • Yeremiya 48:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Ponena za Mowabu+ Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti:+ “Tsoka Nebo+ chifukwa wafunkhidwa! Mzinda wa Kiriyataimu+ walandidwa ndipo anthu ake achita manyazi. Anthu okhala m’malo okwezeka achitetezo achita manyazi ndipo achita mantha.+

  • Ezekieli 25:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti Mowabu+ ndi Seiri+ anena kuti: “Taonani! Nyumba ya Yuda ili ngati mitundu ina yonse ya anthu,”+

  • Amosi 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Yehova wanena kuti, ‘“Popeza kuti Mowabu+ anapanduka mobwerezabwereza, sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anatentha mafupa a mfumu ya Edomu kuti apeze laimu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena