Yesaya 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni.+ Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha Nebo+ ndi Medeba.+ Anthu onse a mmenemo ameta mipala.+ Ndevu za munthu aliyense zametedwa. Yesaya 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako zinaoneka kuti Mowabu anatopa pamalo okwezeka,+ ndipo anapita kumalo opatulika kukapemphera+ koma sizinathandize.+
2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni.+ Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha Nebo+ ndi Medeba.+ Anthu onse a mmenemo ameta mipala.+ Ndevu za munthu aliyense zametedwa.
12 Kenako zinaoneka kuti Mowabu anatopa pamalo okwezeka,+ ndipo anapita kumalo opatulika kukapemphera+ koma sizinathandize.+