Numeri 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho tiyeni tiwalase.Ndithu Hesiboni adzafafanizika mpaka ku Diboni,+Amayi adzaphedwa mpaka ku Nofa, amuna mpaka ku Medeba.”+ Yoswa 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Dziko lawo linayambira ku Aroweli,+ mzinda umene uli m’mphepete mwa chigwa cha Arinoni, ndiponso mzinda umene uli pakati pa chigwacho. Dzikoli linaphatikizapo malo onse okwererapo apafupi ndi Medeba,+
30 Choncho tiyeni tiwalase.Ndithu Hesiboni adzafafanizika mpaka ku Diboni,+Amayi adzaphedwa mpaka ku Nofa, amuna mpaka ku Medeba.”+
16 Dziko lawo linayambira ku Aroweli,+ mzinda umene uli m’mphepete mwa chigwa cha Arinoni, ndiponso mzinda umene uli pakati pa chigwacho. Dzikoli linaphatikizapo malo onse okwererapo apafupi ndi Medeba,+