-
Yoswa 13:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Dera lawo linayambira ku Aroweli, mzinda umene uli mʼmbali mwa chigwa cha Arinoni, ndiponso mzinda umene uli pakatikati pa chigwacho komanso malo onse okwera a Medeba.
-