Yoswa 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Dziko lawo linayambira ku Aroweli,+ mzinda umene uli m’mphepete mwa chigwa cha Arinoni, ndiponso mzinda umene uli pakati pa chigwacho. Dzikoli linaphatikizapo malo onse okwererapo apafupi ndi Medeba,+
16 Dziko lawo linayambira ku Aroweli,+ mzinda umene uli m’mphepete mwa chigwa cha Arinoni, ndiponso mzinda umene uli pakati pa chigwacho. Dzikoli linaphatikizapo malo onse okwererapo apafupi ndi Medeba,+