Yoswa 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Hesiboni,+ ndi midzi yake yonse+ imene inali m’malo okwererapowo. Linaphatikizaponso Diboni,+ Bamoti-baala,+ Beti-baala-meoni,+ Yeremiya 48:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Tsika pamalo ako aulemerero ndipo ukhale ndi ludzu, iwe mwana wamkazi wokhala+ ku Diboni+ chifukwa wowononga Mowabu wabwera kudzakuukira. Iye adzasandutsa bwinja malo ako a mipanda yolimba kwambiri.+
17 Hesiboni,+ ndi midzi yake yonse+ imene inali m’malo okwererapowo. Linaphatikizaponso Diboni,+ Bamoti-baala,+ Beti-baala-meoni,+
18 “Tsika pamalo ako aulemerero ndipo ukhale ndi ludzu, iwe mwana wamkazi wokhala+ ku Diboni+ chifukwa wowononga Mowabu wabwera kudzakuukira. Iye adzasandutsa bwinja malo ako a mipanda yolimba kwambiri.+