Yesaya 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni,+Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha zimene zachitikira Nebo+ ndi Medeba.+ Mutu uliwonse aumeta mpala+ ndipo ndevu zonse zametedwa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:2 Yesaya 1, ptsa. 193-194
2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni,+Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha zimene zachitikira Nebo+ ndi Medeba.+ Mutu uliwonse aumeta mpala+ ndipo ndevu zonse zametedwa.+