Yesaya 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi Kalino+ sali ngati Karikemisi?+ Kodi Hamati+ sali ngati Aripadi?+ Kodi Samariya+ sali ngati Damasiko?+ Yesaya 36:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Musamvere Hezekiya chifukwa akukunyengererani+ ndi mawu akuti, ‘Yehova atilanditsa.’ Kodi pali mulungu wa mitundu ina amene wakwanitsa kupulumutsa mtundu wake m’manja mwa mfumu ya Asuri?+
9 Kodi Kalino+ sali ngati Karikemisi?+ Kodi Hamati+ sali ngati Aripadi?+ Kodi Samariya+ sali ngati Damasiko?+
18 Musamvere Hezekiya chifukwa akukunyengererani+ ndi mawu akuti, ‘Yehova atilanditsa.’ Kodi pali mulungu wa mitundu ina amene wakwanitsa kupulumutsa mtundu wake m’manja mwa mfumu ya Asuri?+