12 Kodi milungu+ ya mitundu imene makolo anga anaiwononga inawalanditsa? Kodi inalanditsa Gozani,+ Harana,+ Rezefi ndi ana a Edeni+ amene anali ku Tela-sara?+
11 kodi sizidzachitika kuti monga momwe ndidzachitire kwa Samariya ndi kwa milungu yake yopanda phindu,+ ndi mmenenso ndidzachitire kwa Yerusalemu ndi kwa mafano ake?’+
12 Kodi milungu+ ya mitundu imene makolo anga anaiwononga inawalanditsa?+ Kodi inalanditsa Gozani,+ Harana,+ Rezefi ndi ana a Edeni+ amene anali ku Tela-sara?