Ekisodo 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ponena za ana a Isiraeli, Farao adzati, ‘Asokonezeka ndipo akungoyendayenda m’dziko lathu. Chipululu chawatsekera.’+ Ekisodo 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mdaniyo anati, ‘Ndiwathamangira,+ ndi kuwapeza!+Ndigawa chuma chawo.+ Pamenepo moyo wanga ukhutira ndi zimene ndawachita!Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+ Salimo 71:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo akunena kuti: “Mulungu wamusiya.+Mulondoleni ndi kumugwira pakuti palibe womulanditsa.”+ Yesaya 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ine ndine Yehova. Dzina langa ndi limeneli,+ ndipo sindidzapereka ulemu wanga kwa wina aliyense+ kapena kupereka ulemerero wanga+ kwa zifaniziro zogoba.+
3 Ndiyeno ponena za ana a Isiraeli, Farao adzati, ‘Asokonezeka ndipo akungoyendayenda m’dziko lathu. Chipululu chawatsekera.’+
9 Mdaniyo anati, ‘Ndiwathamangira,+ ndi kuwapeza!+Ndigawa chuma chawo.+ Pamenepo moyo wanga ukhutira ndi zimene ndawachita!Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+
8 “Ine ndine Yehova. Dzina langa ndi limeneli,+ ndipo sindidzapereka ulemu wanga kwa wina aliyense+ kapena kupereka ulemerero wanga+ kwa zifaniziro zogoba.+