2 Mbiri 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi simukudziwa zimene ineyo ndi makolo anga tinachita kwa anthu onse a mayiko ena?+ Kodi milungu+ ya mitundu ya mayiko ena inatha kupulumutsa mayiko awo m’manja mwanga? Salimo 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuti pasapezeke wondikhadzulakhadzula ngati mmene mkango umachitira,+Pasapezeke wondikwatula popanda wondilanditsa.+ Mateyu 27:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 “Ena anatha kuwapulumutsa, koma kuti adzipulumutse yekha zikumukanika! Ameneyutu ndi Mfumu+ ya Isiraeli, atsiketu pamtengo wozunzikirapowo kuti ife timukhulupirire.+
13 Kodi simukudziwa zimene ineyo ndi makolo anga tinachita kwa anthu onse a mayiko ena?+ Kodi milungu+ ya mitundu ya mayiko ena inatha kupulumutsa mayiko awo m’manja mwanga?
2 Kuti pasapezeke wondikhadzulakhadzula ngati mmene mkango umachitira,+Pasapezeke wondikwatula popanda wondilanditsa.+
42 “Ena anatha kuwapulumutsa, koma kuti adzipulumutse yekha zikumukanika! Ameneyutu ndi Mfumu+ ya Isiraeli, atsiketu pamtengo wozunzikirapowo kuti ife timukhulupirire.+