2 Mafumu 18:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kodi pali mulungu wa mitundu ina amene wakwanitsa kupulumutsa+ mtundu wake m’manja mwa mfumu ya Asuri?+ 2 Mafumu 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atentha milungu yawo pamoto, chifukwa sinali milungu,+ koma ntchito ya manja a anthu,+ mitengo ndi miyala, n’chifukwa chake anaiwononga. Salimo 115:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amene amawapanga adzafanana nawo.+Onse amene amawakhulupirira adzakhala ngati mafanowo.+ Yesaya 44:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu inu musachite mantha ndipo musathedwe nzeru.+ Kodi sindinachititse aliyense wa inu kuti amve kuyambira nthawi imeneyo? Kodi sindinakuuzeni zimenezi?+ Inu ndinu mboni zanga.+ Kodi palinso Mulungu kupatulapo ine?+ Ayi, palibe Thanthwe.+ Sindikudziwapo aliyense.’”
33 Kodi pali mulungu wa mitundu ina amene wakwanitsa kupulumutsa+ mtundu wake m’manja mwa mfumu ya Asuri?+
18 Atentha milungu yawo pamoto, chifukwa sinali milungu,+ koma ntchito ya manja a anthu,+ mitengo ndi miyala, n’chifukwa chake anaiwononga.
8 Anthu inu musachite mantha ndipo musathedwe nzeru.+ Kodi sindinachititse aliyense wa inu kuti amve kuyambira nthawi imeneyo? Kodi sindinakuuzeni zimenezi?+ Inu ndinu mboni zanga.+ Kodi palinso Mulungu kupatulapo ine?+ Ayi, palibe Thanthwe.+ Sindikudziwapo aliyense.’”