Deuteronomo 4:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Inu mukudziwa bwino lero, ndipo muzikumbukira m’mitima yanu, kuti Yehova ndiye Mulungu woona, kumwamba ndiponso padziko lapansi.+ Palibenso wina.+ 1 Samueli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Palibe woyera ngati Yehova. Palibe aliyense koma inu nokha.+Palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+
39 Inu mukudziwa bwino lero, ndipo muzikumbukira m’mitima yanu, kuti Yehova ndiye Mulungu woona, kumwamba ndiponso padziko lapansi.+ Palibenso wina.+
2 Palibe woyera ngati Yehova. Palibe aliyense koma inu nokha.+Palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+