Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+ Deuteronomo 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, inu ndinu amene mwayamba kuchititsa atumiki anu kuti aone ukulu wanu+ ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Ndi mulungu winanso uti, kumwamba kapena padziko lapansi, amene akuchita ntchito ngati zanu, ndiponso ntchito zamphamvu ngati zanu?+ Deuteronomo 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Inuyo mwasonyezedwa zinthu zimenezi kuti mudziwe kuti Yehova ndiye Mulungu woona,+ ndipo palibenso wina.+ Salimo 73:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Winanso ndani kumwambako amene ali kumbali yanga?+Palibe wina wondisangalatsa padziko lapansi koma inu nokha.+ Salimo 86:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu.+Ndipo palibe ntchito zilizonse zofanana ndi ntchito zanu.+ Salimo 89:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndani kumwamba angayerekezeredwe ndi Yehova?+Ndani angafanane ndi Yehova pakati pa ana a Mulungu?+
11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+
24 ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, inu ndinu amene mwayamba kuchititsa atumiki anu kuti aone ukulu wanu+ ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Ndi mulungu winanso uti, kumwamba kapena padziko lapansi, amene akuchita ntchito ngati zanu, ndiponso ntchito zamphamvu ngati zanu?+
35 Inuyo mwasonyezedwa zinthu zimenezi kuti mudziwe kuti Yehova ndiye Mulungu woona,+ ndipo palibenso wina.+
25 Winanso ndani kumwambako amene ali kumbali yanga?+Palibe wina wondisangalatsa padziko lapansi koma inu nokha.+
8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu.+Ndipo palibe ntchito zilizonse zofanana ndi ntchito zanu.+
6 Pakuti ndani kumwamba angayerekezeredwe ndi Yehova?+Ndani angafanane ndi Yehova pakati pa ana a Mulungu?+